Description

Welcome to Blessings Khakhi Mobile money Services. Ndine agent wa Airtel money komaso Mpamba. Ndikupezeka panja pa Mzuzu university along M1. Kiosk yanga ili mphepete mwa mseu wa M1 maka maka pa T-junction yolowera ku Viyere CCAP Church.

Ndimagulisaso ma number a nyuwani komaso kubwezelesa ma number otaika.

Advertising Opportunity---TSATSANI MALONDA PA PAGE YANGA PANO

Page yangayi imalandira ma customer ochuluka tsiku ndi tsiku kuzasuzumila ngati ndalama zilipo kapena ayi. Anthu ochokera ku Mzuzu University ndi madera ozungulira ndi akabwele bwele pa page yangayi moti ngati mufuna kuti malonda anu afikire anthu mwa changu ikani pa page yangayi.

MTENGO---PRICING

Page yangayi pali malo khumi (10) omwe mutha kuitanilapo malonda anu mosavuta ndipo mtengo ndi 100 kwacha yokha pa tsiku.

Malonda anu tizawaika kuchokera mamawa 6am kufikiraso 6pm mazulo.

FOMART---MTUNDU WA PIKICHA YAMALONDA

Timalora mtundu wa jpeg/png/gif

SIZE

Pikicha/images/posters must be 2Mb or less.

CONTACT INFORMATION

Mutha kutipeza pa number iyi: 0986007317

Zikomo

Location
AIRTEL MONEY

AVAILABLE, -WITHDRAWAL ONLY, UPTO 300 000

TNM MPAMBA

AVAILABLE, -WITHDRAWAL AND DEPOSITS, UPTO 300 000

MUKURU

AVAILABLE, -WITHDRAWAL ONLY, UPTO 300 000

HELLO PAISA

AVAILABLE

STD BANK KWACHA POINT

UNAVAILABLE

NBM FAST SERVE

UNAVAILABLE

Open
Open hours today: 6:00 am - 6:00 pm Toggle weekly schedule
  • Monday

    6:00 am - 6:00 pm

  • Tuesday

    6:00 am - 6:00 pm

  • Wednesday

    6:00 am - 6:00 pm

  • Thursday

    6:00 am - 6:00 pm

  • Friday

    6:00 am - 6:00 pm

  • Saturday

    6:00 am - 6:00 pm

  • Sunday

    By appointment only

  • April 4, 2026 6:11 am local time

Contact business

Error: Contact form not found.

FCB SIMPO CASH

UNAVAILABLE

NBS BANK PAFUPI

UNAVAILABLE

FDH BANK PAKHOMO

AVAILABLE

CENTENARY BANK PAKWATHU

UNAVAILABLE

  • No comments yet.
  • Add a review